Mu Baibulo, kwalembedwa,
“Hava adzakhala mayi wa amoyo onse”
“Sara adzakhala mayi wa amitundu,” ndi
“Yerusalemu wa Kumwamba ndi Amayi athu auzimu.”
Njira ya chipulumutso ndi kukhulupirira mwa Mulungu Atate
ndipo Mulungu Amayi pomvera mawu a m'Baibulo.
Mamembala a Mpingo wa Mulungu amene amakhulupirira Mzimu Woyera Ahnsahnghong, amene anakwaniritsa maulosi onse a m'Baibulo, ndi Mulungu Amayi, amene ali Mkwatibwi Wake, ndi anthu anzeru amene amaopa Mulungu ndi kumanga nyumba zawo pathanthwe.
nanena, Idza kuno, ndidzakuonetsa mkwatibwi,
mkazi wa Mwanawankhosa.
. . . nandionetsa mzinda wopatulikawo, Yerusalemu,
wotsika m'Mwamba kuchokera kwa Mulungu, Civumbulutso 21:9–10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi