M'dziko lino lodzaza ndi masoka osiyanasiyana ndi matenda opatsirana,
iwo amene angatipatse chiyembekezo cha Ufumu Wamuyaya Wakumwamba
kumene kulibe mavuto, kuzunzika, kapena imfa, ndi Atate Akumwamba
ndi Amayi amene anabwera ngati Mzimu ndi Mkwatibwi.
Monga Mulungu adalola anthu ake kuzindikira Khristu
kudzera mu Pangano lakale, Iye adatiphunzitsa momwe tingazindikirire
Amayi athu Akumwamba kudzera mu Pangano Latsopano mu m'badwo uno.
Anthu omwe amakhala opanda osataya chiyembekezo nthawi zonse,
pokhala odzala ndi kuthokoza, ndiwo anthu a Mpingo wa Mulungu.
Amatsatira ziphunzitso za Amayi Akumwamba ndikusunga Pangano Latsopano.
Izo ndizo zophiphiritsa; pakuti akaziwa ali mapangano awiri. . . Koma Yerusalemu wa kumwamba uli waufulu, ndiwo amai wathu. Agalatiya 4:24–26
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi