Mulungu anapatsa Uthenga Wabwino wa Ufumu
kwa iwo amene anavomereza kuti, “Khalani mboni zanga.
Mukhale antchito a Pangano Latsopano.”
Mulungu anawalonjeza dalitso lolandirani Ufumu
wa Kumwamba, amene ngalandire cholowa cha Mulungu.
Monga momwe Gideon anapambana pankhondo ataswa mitsuko ndikuonetsera kuwala,
ntchito yodabwitsa ya Mzimu Woyera monga ulaliki wa Mpingo woyambirira udzachitika mu m'badwo uno, pamene tionetsera ulemerero wa Yerusalemu Amayi a Kumwamba kudzera mu kuwala kwa choonadi cha pangano latsopano.
Popeza sitingathe kubwera ku chipulumutso kupyolera mu malamulo a anthu,
koma kudzera mu Uthenga Wabwino wa Mulungu, Mpingo wa Mulungu ukusunga malamulo a Mulungu amene Khristu Ahnsahnghong wabwezeretsa, ndipo ukugwira ntchito yake ngati mboni za Mulungu kwathunthu
Ndipo ananena nao, Mukani kudziko lonse lapansi,
lalikirani Uthenga Wabwino kwa olengedwa onse.
Amene akhulupirira nabatizidwa, adzapulumutsidwa;
koma amene sakhulupirira adzalangidwa. Marko 16:15–16
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi