Kuyambira pachiyambi, Mulungu anapanga dongosolo la chipulumutso chathu pa kugawa mibadwo kukhala M’badwo wa Atate, wa Mwana, ndi wa Mzimu Woyera, ndipo analola iwo amene amapembeza ndi kupemphera m’dzina loyenera la Mpulumutsi mu m’badwo uliwonse kulandira chipulumutso cha Mulungu.
Ndi okhawo amene alandira Khristu Ahnsahnghong, dzina latsopano la Yesu, ndi Yerusalemu Watsopano Mulungu Amayi monga Mpulumutsi mu Nyengo ya Mzimu Woyera ndi amene angalandire chipulumutso, monga momwe Mose anavomerezera Yehova monga Mpulumutsi ndipo Mpingo woyamba unavomereza Yesu monga Mpulumutsi.
Iye wakupambana, ndidzamyesa iye mzati wa m'Kachisi wa Mulungu wanga, ndipo kutuluka sadzatulukamonso; ndipo ndidzalemba pa iye dzina la Mulungu wanga, ndi dzina la mzinda wa Mulungu wanga, la Yerusalemu watsopano, wotsika m'Mwamba, kuchokera kwa Mulungu wanga; ndi dzina langa latsopano.
Chivumbulutso 3:12
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi