Ngakhale kuti dzina la Mulungu ndi maonekedwe ake zimasiyana mu m’bado uliwonse, Baibulo limachitira umboni momveka bwino kuti Mulungu Atate Yehova, Mulungu Mwana Yesu, ndi Mulungu Mzimu Woyera Ahnsahnghong ndi Mulungu mmodzi.
Monga momwe Petro ndi Paulo anazindikirira Yesu amene anadza m’thupi mu M’badwo wa Mwana, mamembala a Mpingo wa Mulungu amatsatira ziphunzitso za Mulungu Ahnsahnghong amene anabwera mu M’badwo wa Mzimu Woyera mogwirizana ndi maulosi a m’Baibulo.
Pakuti kwa ife mwana wakhanda wabadwa, kwa ife mwana wamwamuna wapatsidwa; ndipo ulamuliro udzakhala pa phewa lake, ndipo adzamutcha dzina lake Wodabwitsa, Wauphungu, Mulungu wamphamvu, Atate Wosatha, . . .
Yesaya 9:6
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi