Mu dziko lino, pali magulu awiri a anthu:
iwo mene akumva ndi kuchita zomwe Mulungu akunena,
ndi iwo omwe sangathe kumvetsetsa ngakhale amva mawu a Mulungu mochuluka bwanji.
Mu m’badwo wotsiriza wa Mzimu Woyera, pali malo
komwe titha kumva ndikumvetsetsa mawu
a Atate Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi,
ndi kusunga Paskha ndi Sabata Langano Latsopano
molingana ndi zitsanzo za Mulungu.
Malowa ndi World Mission Society Church of God.
“koma inu simukhulupirira chifukwa simuli a gulu lankhosa zanga. Nkhosa zanga zimamva mawu anga, Ine ndimazidziwa, ndipo zimanditsata Ine.” [Yohane 10:26–27]
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi