Mulungu adalenga Hava (moyo) pa tsiku lachisanu ndi chimodzi ku ntchito yake yakulenga, ndipo adalola kuti zinthu zonse zizilandira moyo kuchokera kwa amayi awo. Izi zikusonyeza kuti Mulungu Amayi ndi amene amapereka moyo wosatha kwa anthu.
Monga momwe ana obadwa amatengera mitochondria kuchokera kwa amayi awo ndi kulandira moyo, tikhoza kulandira moyo wosatha kudzera mwa Mulungu Amayi mu M'badwo wa Mzimu Woyera monga taonera mu vumbulutso la angelo adamuwonetsera Yohane.
Ndipo anadza mmodzi wa angelo asanu ndi awiri akukhala nazo mbale zisanu ndi ziwiri, zodzala ndi miliri yotsiriza isanu ndi iwiri; ndipo analankhula ndi ine, nanena, Idza kuno, ndidzakuonetsa mkwatibwi, ... nandionetsa mzinda wopatulikawo, Yerusalemu, wotsika m'Mwamba kuchokera kwa Mulungu.
Chivumbulutso 21:9-10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi