Zaka 2,000 zapitazo, mtumwi Paulo analalikira kwa anthu amene ankalambira mwakhungu mulungu wosadziwika kuti Yesu Khristu ndi Mulungu amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi. Momwemonso, lero, tiyenera kuyesetsa kudziwa ndi kukhulupirira mwa Mzimu ndi Mkwatibwi amene abwera kudzapulumutsa anthu.
M’Baibulo,mau akuti Mulungu analembedwa koposa ka 2,500 ngati dzina lochulukitsa lakuti Elohimu. Monga momwe tingawonere kuti atate ndi amayi amakhala pamodzi m’dongosolo la banja lolengedwa mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, Mulungu yemweyonso amene amachitiridwa umboni m’Baibulo ndi Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi.
Pakati pa mipingo yambiri padziko lapansi, mpingo wokhawo umene umakhulupirira Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi ndi Mpingo wa Mulungu wa Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse.
Tidziwe tsono; tilondole kudziwa Yehova. Kutuluka kwake Kwakonzekeratu, ngati matanda kucha; ndipo adzatidzera ngati mvula, ngati mvula ya masika . . .
Hoseya 6:3
amene atumikira chifaniziro ndi mthunzi wa zakumwambazo monga. . . .
Ahebri 8:5
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi