Ngati ndife a chilombo, tidzalandira chizindikiro cha chilombo, chomwe chimatsogolera ku chilango cha gehena. Tidzalandira chizindikiro cha chipulumutso kuchokera kwa Mulungu pamene tizindikira ndi kukhala ndi chikhulupiriro cholimba mwa Khristu Ahnsahnghong, dzina latsopano la Yesu, ndi Yerusalemu Watsopano Amayi wa Kumwamba.
Baibulo limaneneratu kuti ntchito yaikulu ya Mulungu idzakhala kuika chidindo chake pamphumi pa ana ake, kuyambira kumalekezero a dziko lapansi kuchokera ku Republic of Korea, kumene dzuŵa limatuluka, kudzera m’malamulo Ake kuphatikizapo la Paskha.
Ndipo ndinaona chilombo chilinkutuluka m'nyanja… ndipo chinjoka chinampatsa iye mphamvu yake… Ndipo chichita kuti onse,… alandire chilembo padzanja lao ndi pamphumi pao; ndi kuti munthu sangakhoze kugula kapena kugulitsa, koma iye yekha wakukhala nacho chilembo, ndilo dzina la chilombo, kapena chiwerengero cha dzina lake.
Chivumbulutso 13:1-17
Ndipo ndinaona mngelo wina, anakwera kuchokera potuluka dzuwa, ali nacho chizindikiro cha Mulungu wamoyo: ndipo anafuula ndi mau aakulu kuitana angelo anai, amene adalandira mphamvu kuipsa dziko ndi nyanja, 3nanena, Musaipse dziko, kapena nyanja, kapena mitengo, kufikira tidasindikiza chizindikiro akapolo a Mulungu wathu, pamphumi pao.
Chivumbulutso 7:2-3
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi