Monga moyo ndi madzi ndizogwirizana padziko lapansi, kuti ife tilandire moyo wosatha ndipo moyo mosangalala mu Ufumu wa Kumwamba, ife tiyenera kulandira madzi a moyo.
Popeza Mzimu ndi Mkwatibwi anatiuza kuti tilandire madzi a moyo, tiyenera kuzindikira ndi kukhulupirira mu Mzimu ndi Mkwatibwi ndikulandira madzi a moyo.
Baibulo limachitira umboni kuti Mulungu Ahnsahnghong ndi Amayi athu Akumwamba ndiye Mzimu ndi Mkwatibwi. Mulungu amatipatsa madzi amoyo mu Mpingo wa Mulungu komwe Amakhala.
Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena, Idzani. Ndipo wakumva anene, Idzani. Ndipo wakumva ludzu adze; iye wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere. Civumbulutso 22:17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi