Mulungu adachitira umboni zakupezeka kwa Mulungu Amayi kudzera m’zinthu zonse;
aneneri a m’Baibulo amatiuza kuti anthu akhoza kupulumutsidwa
pokhapokha atabwera kwa Yerusalemu, Amayi a Kumwamba.
Chisomo chapadera chomwe Mulungu wapatsa anthu ake omwe adzapulumuke
ndi dalitso lotsogolera anthu kulowa m’dziko la kuwala
powonetsa ulemerero wa Mulungu Amayi kudziko lam’dima lino lopanda chowonadi.
Ndipo anati Mulungu, Tipange munthu m’chifanizo chathu, monga mwa chikhalidwe chathu[.]Mulungu ndipo adalenga munthu m’chifanizo chake, m’chifanizo cha Mulungu adamlenga iye; adalenga iwo mwamuna ndi mkazi. Genesis 1:26–27
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi