Anthu adzayenera kufa ndipo pamapeto pake adzaweruzidwa.
N’chifukwa chake tikuyenera kumvetsetsa chifuniro cha Mulungu
ndi kukhalani moyo wathu kuti tipite Kumwamba.
Atate Akumwamba ndi Amayi Akumwamba anabwera padziko lapansi
okha kuti atipulumutse ku zowawa za Gehena, zomwe ndizopweteka kwambiri
kuposa matenda a Complex Regional Pain Syndrome, ndipo Iwo adakhazikitsa
Mpingo wa Mulungu ndipo adapereka choonadi cha moyo kwa ife.
Ndipo popeza kwaikikatu kwa anthu kufa kamodzi, ndipo atafa, chiweruziro; kotero Khristunso ataperekedwa nsembe kamodzi kukasenza machimo a ambiri, adzaonekera pa nthawi yachiwiri, wopanda uchimo, kwa iwo amene amlindirira, kufikira chipulumutso.
Ahebri 9:27–28
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi