Mulungu adakonza zonse pa chipulumutso
cha anthu akumwamba ngakhale asanalenge dziko lapansi.
Adakonzera chombo pamaso pa chiweruziro
ndi madzi mu nthawi ya Nowa; Adakonzera mphepo
yakum’mawa kugawa Nyanja Yofiyira m’nthawi ya Mose;
Adakonzera mana ndi madzi kwa Aisrayeli muulendo wamchipululu;
Adakonzekeretsa Paskha wa chipangano chatsopano
kupulumutsa anthu akumwamba m’masiku otsiriza.
Ndi okhawo omwe amasunga Paskha wa pangano latsopano,
lomwe Mulungu adalikonzera asanalenge dziko lapansi,
angathe kukhala anthu a Mulungu ndi kukhala nzika zakumwamba,
wokhala ndi chisindikizo cha chiwombolo.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi