Tiyenera kumvetsetsa osati dziko lapansi lokha,
komanso dziko la uzimu kuti tipeze cholinga cha moyo wathu
ndi kulandira chipulumutso.
Pofuna kupulumutsa anthu, omwe kuyenera kufa
chifukwa cha machimo omwe anachimwa ku dziko la angelo,
Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi
abwera ku dziko lapansi lino ndi kukhazikitsa
Paskha Pangano Latsopano mu Mpingo wa Mulungu.
“Pakuti Mwana wa Munthu anadza kufunafuna
ndi kupulumutsa chotayikacho”. Luka 19:10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi