Aisraele amene anayenda mchipululu kwa zaka 40 anaiwala za chozizwitsa cha Nyanja Yofiira ndi mphamvu ya Paskha Mulungu anaonetsa iwo, ndipo potsiriza anawonongedwa popeza ankangoyang'ana pa miyoyo yawo.
Mulungu anati, “Chilichonse chimene sichibwera m'chikhulupiriro, ndicho uchimo.”
Zikutanthauza kuti pokha pokha titakhala ndi chikhulupiriro ndi kumvera ziphunzitso ndi malamulo a Mulungu, sitingathe kulandira chipulumutso pamapeto.
Mamembala a mpingo wa Mulungu samasuntha muchina chilichonse nthawi zonse chifukwa chakuti ali ndi chikhulupiriro mtheradi mwa Mulungu Atate Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, amene anadza mu M'badwo wa Mzimu Woyera.
Dziyeseni nokha, ngati muli m'chikhulupiriro, dzitsimikizeni nokha. 2 Akorinto 13:5
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi