Pokhapokha tikamvetsetsa zinsinsi za Mtengo wa Moyo
mu Edeni, likasa la Chipangano ndi Paskha Pangano
Latsopano tingamasulidwa ku uchimo
ndi kulowa Ufumu wosatha wa Kumwamba.
Mulungu anabwera ku dziko lapansi kachiwiri kubweretsa chipulumutso
kwa anthu.Apulumutsi mu M’badwo wa Mzimu Woyera,
amene anabwedzeretsa Paskha wa Pangano Latsopano
-choonadi chenicheni cha Mtengo wa moyo-
ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Yesu anayankhula zinthu zonsezi kwa gulu la anthu mʼmafanizo ndipo Iye sananene kalikonse kwa iwo osagwiritsa ntchito fanizo. . . . “. . . ndidzawulula zinthu zobisika chiyambire kukhazikidwa kwa dziko lapansi.” Mateyu 13:34–35
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi