Ntchito ya Mzimu Woyera inachitika ndi Mzimu Woyera womwe unatsanulidwa pa mpingo woyambirira pa Tsiku la Pentekoste. Kudzera mwa izi, anthu 3,000 ndi 5,000 adalapa tsiku limodzi, ndipo chowonadi chakuti Yesu ndiye Khristu chidafalikira mwachangu ngakhale kumayiko a Achikunja.
Lero, Mpingo wa Mulungu womwe umasunga Phwando la Misasa ukugwira Ntchito Yodabwitsa ya Mzimu Woyera kuchitira umboni padziko lonse lapansi za Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, omwe ndiwo Apulumutsi mu M’badwo wa Mzimu Woyera.
Komatu mudzalandira mphamvu, Mzimu Woyera atadza pa inu: ndipo mudzakhala mboni zanga mu Yerusalemu, ndi mu Yudeya monse, ndi mu Samariya, ndi kufikira malekezero ake a dziko. Machitidwe 1:8
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi