Ngati ndinu Mkhristu, muyenera kugwira ntchito mwakhama kuti mukhale padziko lapansi pano, koma koposa zonse, muyenera kukhala ndi ulemerero wamuyaya osati chisangalalo cha kanthaŵi pamene mukuphunzira tsiku ndi tsiku za moyo wosatha wa Kumwamba kudzera m’mawu a Mulungu.
Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi apatsa anthu madalitso a Pangano Latsopano, ndiko kuti, Kumwamba kumene tidzasangalala ndi moyo wosatha ndi ulemerero, osati ulemerero wosakhalitsa ndi wosowa. Choncho, monga Mtumwi Paulo, mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhala antchito a Pangano Latsopano ndikukhala moyo wa Mkhristu weniweni, umene Mulungu amakondwera nawo.
Ndani adziwa mphamvu ya mkwiyo wanu?
. . . Tiphunzitseni kuwerenga bwino masiku athu, kuti tipeze mtima wanzeru.
Salmo 90:11–12
Anatikwaniritsa kukhala atumiki a pangano latsopano, losati la chilembo, koma la Mzimu;
pakuti chilembo chimapha, koma Mzimu apatsa moyo.
2 Akorinto 3:6
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi