Kudzera m’Baibulo, Mulungu adatiphunzitsa momwe tingakhalire moyo wamtengo wapata womwe umatilola ife kulandira ulemerero wa Kumwamba.
Monga madzi ndi ofunika kwambiri kuposa golide woyenga bwino mu chipululu ndi m’busa ndi ofunika kwambiri kuposa mfumu kwa nkhosa yosochera, ziwalo za Mpingo wa Mulungu, amalemekeza ziphunzitso za Pangano Latsopano monga Sabata ndi Paska,zomwe zitha kutsogolera ife ku Ufumu Wakumwamba..
Ndipo popeza kwaikikatu kwa anthu kufa kamodzi, ndipo atafa, chiweruziro; kotero Khristunso . . . adzaonekera pa nthawi yachiwiri, wopanda uchimo, kwa iwo amene amlindirira, kufikira chipulumutso. [Ahebri 9:27–28]
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi