Bwilibwisa ya tomboliro itha kuwoneka yoyipa kwambiri koma munthawi yake, imatuluka pakhungu ndikutsegula mapiko ake asiliva. Momwemonso, thupi la munthu, limafunanso kuti lisinthidwe likhale thupi lauzimu lomwe limafanana ndi Mulungu pophunzira kuganizila komanso kukonda Mulungu.
Tsiku la Kuuka kwa akufa siliri tsiku lokondwerera kuuka kwa Yesu. Ili ndi tsiku lothokoza Mulungu kuchokera pansi pamtima chifukwa chopatsa chiyembekezo cha kuuka kwa akufa kwa mtundu wa anthu omwe adzafa, komanso kutibwezetsa ku moyo wosafa.
Taonani, ndikuuzani chinsinsi; sitidzagona tonse, koma tonse tidzasandulika, m’kamphindi m’kutwanima kwa diso, palipenga lotsiriza. 1 Akorinto 15:51
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi