Yesu adafera pamtanda chifukwa cha machimo a anthu ndipo adaukitsidwa kwa akufa tsiku lachitatu atapachikidwa. Kudzera mwa kuuka Kwake, Adatsimikiza kuti pali kuuka ndi kusandulika kwa anthu, nawonso.
Gulu La Utumiki Wa Dziko Lonse la Mpingo Wa Mulungu limakhulupirira lonjezo la Mulungu kuti matupi a anthu adzasandulika n’kukhala matupi auzimu monganso pali zolengedwa zomwe zimasintha m’chilengedwe monga atombolombo ndi nyenje. Mpingo wa Mulungu, womwe Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi akutsogolera, umatenga nawo gawo m’lonjezo la chipulumutso.
“Pakuti ufulu wathu uli Kumwamba; kuchokera komwenso tilindirira Mpulumutsi, Ambuye Yesu Khristu; amene adzasanduliza thupi lathu lopepulidwa, lifanane nalo thupi lake la ulemerero, monga mwa machitidwe amene akhoza kudzigonjetsera nao zinthu zonse.” Afilipi 3:20–21
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi