Malinga ndi ulosi wa chikondwerero cha Zipatso Zoyambirira, Yesu anaukitsidwa Lamlungu monga chipatso choyamba cha iwo amene anali atagona. Tsiku lomwe Iye anaswa mphamvu ya imfa, kupatsa anthu chiyembekezo cha kuuka, linali Tsiku la kuuka kwa akufa.
Mulungu Ahnsahnghong ndi Amayi Akumwamba adabwera padziko lapansi kudzapatsa anthu chiyembekezo cha kuuka ndikubwezeretsanso mawonekedwe athu aungelo.
Potsatira zomwe Baibulo limaphunzitsa, anthu ayenera kusunga Tsiku La kuuka kwa akufa Lamlungu mwa kunyema mkate, osati mazira, kutsegula maso athu auzimu.
Koma nʼzoonadi kuti Khristu anaukitsidwa kwa akufa, chipatso choyamba cha onse ogona tulo. 1 Akorinto 15:20
Ife timakhulupirira kuti Yesu anamwalira naukanso…ndipo akufa amene ali mwa Yesu adzauka poyamba. Kenaka, ife amene tili ndi moyo, otsalafe, tidzakwatulidwa pamodzi ndi iwo mʼmitambo kukakumana ndi Ambuye mlengalenga. 1 Atesalonika 4:14–17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi