Panali wogwira ntchito wamba ku kampani
ya Rockefeller, yemwe adadzitamandira
kwambiri ndi zomwe kampaniyo idapanga
kotero kuti adatchedwa “Mtsuko wamafuta, $4.”
Kenako anakhala pulezidenti wa kampaniyo.
Kupyolera mu nkhani yake, tikhoza kumvetsetsa
kuti pamene tidzitamandira za Khristu Ahnsahnghong
ndi Mulungu Amayi amene abwera monga Apulumutsi
mu nthawi ya Mzimu Woyera ndi kulalikira choonadi
cha chipulumutso, tidzakhala oyenerera kulowa mu ufumu wakumwamba.
Ana a Mulungu sayenera kutengeka ndi
maganizo a anthu ena, kapena kutengera
makhalidwe a m’dzikoli.
Ayenera kungoyang’ana maganizo a Mulungu
ndi kuyamikira ntchito yolalikira uthenga wabwino.
Pokhapokha, m’pamene angakhale ndi moyo
mogwirizana ndi maulosi, kupeza matalenti
khumi, ndi kuyamikiridwa kuti, “Mwachita bwino!”
[I]wo otembenuza ambiri atsate chilungamo ngati nyenyezi kunthawi za nthawi.
Danieli 12:3
Ndipo masiku onse, mu Kachisi ndi m’nyumba, sanaleke kuphunzitsa ndi kulalikira Khristu Yesu.
Machitidwe 5:42
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi