Mulungu amadziwa chimaliziro kuchokera pachiyambi. Kudzera mu kachilombo ka vairasi komwe sitinakamvepo komwe kanakhudza dziko lonse lapansi komanso nyengo zosiyanasiyana zachilendo, Mulungu akudzutsa ana ake onse lisanadze Tsiku la Chiweruzo, lomwe lifike posachedwa. Akutiphunzitsa kuti ino ndiyo nthawi yodzuka kutulo tathu ndikukonzekera mafuta achikhulupiriro.
Mamembala a Mpingo wa Mulungu amadziwa gwelo la miliri yambiriyi ndipo amazindikira kuti njira yopulumutsidwira pa Tsiku Lachiweruzo ndikuzindikira waniritsa maulosi a m’Baibulo, omwe Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi Akumwamba awulula. Mamembalawo amakhala moyo wolapa ndipo akuyenda kupita ku Ufumu Wakumwamba, kumvera mawu a Mulungu.
“ ‘Mukamva za nkhondo ndi kupanduka, musachite mantha. Zinthu izi ziyenera kuchitika poyamba, koma chimaliziro sichidzafika nthawi yomweyo. ‘Kenako anawauza kuti:’ Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina, ndipo ufumu ndi ufumu wina. Kudzakhala zivomezi zazikulu, njala ndi miliri m’malo osiyanasiyana.’ ”
Luke 21:9–11
“Ndilalikira za chimaliziro kuyambira pachiyambi, ndi kuyambira nthawi zakale, ndinena zinthu zimene zisanachitidwe. Ndi kunena: Uphungu wanga udzakhala, ndipo ndidzachita zofuna zanga zonse.’ ”
Yesaya 46:10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi