Mu chipangano Chakale, Aisraeli anapulumutsidwa kudzera mu mwazi wa mwana wankhosa wa Paska. Izi zikuwonetsa kuti iwo omwe ali ndi mwazi wa Yesu, amene adabwera ngati Mwana wankhosa wa Paska, akhoza kupulumutsidwa ndipo omwe alibe mwazi wake adzalandira masoka.
Tikatenga nawo mbali pamwambo wopatulika wa Paska kudya thupi la Mulungu ndikumwa mwazi wake, masoka adzatipitirira chifukwa Mulungu ali mwa ife. Kuphatikiza apo, titha kusindikizidwa ngati ana a Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi.
“Mzimu yekha achita umboni pamodzi ndi mzimu wathu, kuti tili ana a Mulungu.” Aroma 8:16
“Iye wakudya thupi langa ndi kumwa mwazi wanga ali nao moyo wosatha; ndipo Ine ndidzamuukitsa iye tsiku lomaliza. . . . Iye wakudya thupi langa ndi kumwa mwazi wanga akhala mwa Ine ndi Ine mwa iye.” Yohane 6:54–56
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi