“Iye amene azamanganso mzinda wa Yeriko adzataya mwana wake wamwamuna woyamba kubadwa, ndi mwana wake wamng’ono.”
Ulosi wa Yoswa sunathe ngakhale patapita
zaka 500 koma unakwaniritsidwa.
Monga mwa izi, ulosi uliwonse wolembedwa
m’Baibulo ukukwaniritsidwa, ngakhale wochepa.
“Anthu padziko lapansi adzabwera ku Mpingo wa
Mulungu kudzaphunzira ziphunzitso za Mulungu Amayi.”
Masiku ano, anthu akhoza kuchitira umboni kuti mawu
a Khristu Ahnsahnghong onena za ulemerero wa
Mayi wa Kumwamba Yerusalemu akukwaniritsidwa.
N’chifukwa chakuti mawu ake ndi maulosi a m’Baibulo
amene Mulungu analosera kale kudzera mwa aneneri
ambiri monga Yesaya, Yeremiya, Ezekieli, Zekariya, ndi mtumwi Yohane.
Ndipo tili nao mau a chinenero okhazikika
koposa; amene muchita bwino powasamalira,
monga nyali younikira m'malo a mdima, . . . ndi
kudziwa ichi poyamba, kuti palibe chinenero cha
lembo chitanthauzidwa pa chokha, pakuti kale lonse
chinenero sichinadze ndi chifuniro cha munthu; koma
anthu a Mulungu, ogwidwa ndi Mzimu Woyera, analankhula.
2 Petulo 1:19-21
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi