Pamene kukwera kwa kutentha kwa dziko kukuchititsa kuti masoka achilengedwe ndi matenda achuluke kwambiri, anthu sadziwa choti achite ndiponso sangathe kupereka njira yothetsera vutoli. Ndi Mulungu yekha amene angatiphunzitse njira yopulumutsira ku masoka oterowo.
Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi atikhululukira tchimo lodya zipatso za Mtengo wodziwitsa zabwino ndi zoipa umene unabweretsa imfa pa anthu onse. Iwo atiphunzitsa choonadi cha Paskha wa Pangano Latsopano —njira yopita ku Mtengo wa Moyo. Mpingo wokha umene uli nacho choonadi ichi cha Mtengo wa Moyo lero ndi Mpingo wa Mulungu.
Ndipo anati Yehova Mulungu, Taonani, munthuyo akhala ngati mmodzi wa ife, wakudziwa zabwino ndi zoipa: ndipo tsopano kuti asatambasule dzanja lake ndi kutenga za mtengo wa moyo, ndi kudya, ndi kukhala ndi moyo nthawi zonse.
Genesis 3:22
Chifukwa chake Yesu anati kwa iwo, “Indetu, indetu, ndinena ndi inu . . . Iye wakudya thupi langa ndi kumwa mwazi wanga ali nao moyo wosatha; ndipo Ine ndidzamuukitsa iye tsiku lomaliza.”
Yohane 6:53–54
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi