Pa Tsiku la Chitetezero, Mose adatsika ndi magome amiyala a Malamulo Khumi ndikupereka chifuniro cha Mulungu. Kenako anthu mokondwera anabweretsa zopereka kuti zigwiritsidwe ntchito yomanga kachisi, kuthokoza Mulungu chifukwa chokhululukira machimo awo. Phwando ili ndi Phwando la Misasa.
Mu m’badwo uno, mamembala a Mpingo wa Mulungu akuchita ntchito ya mlaliki posonkhanitsa anthu akumwamba, zipangizo za kachisi za kuuzimu, kuchokera kudziko lonse lapansi ndikuwatsogolera ku chipulumutso cha Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.Iyi ndiyo ntchito yodalitsika ya mamembala a Mpingo wa Mulungu, omwe akukwaniritsa ulosi wa Phwando la Misasa.
“Iye wakupambana ndidzamyesa iye mzati wa m’Kachisi wa Mulungu wanga. Ndipo kutuluka sadzatulukamonso.”
Chivumbulutso 3:12
Chifukwa chake Yehova Mulungu wa makamu atero:”Chifukwa munena mau awa taona, anthu . . . awa ndidzayesa nkhuni . . .”
Yeremiya 5:14
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi