Chisomo cha Mzimu Woyera chimachuluka
paliponse pamene mawu a Mulungu agwiritsidwa
ntchito. Komabe, chisomo chimawola pamene mawu a
Mulungu sanagwiritsidwe ntchito.
Nyanja ya Galileya inakhala nyanja ya
moyo pa kulandira madzi ndipo madziwo ankayenda.
Nyanja Yakufa inakhala nyanja ya
imfa chifukwa imangolandira madzi
kenako n’kuwasunga yokha.
Mu nthawi ya Mzimu Woyera, chisomo cha
Mulungu chikusefukira mu Mpingo wa Mulungu
chifukwa mamembala a kumeneko amalalikira
uthenga wabwino ndi Mzimu Woyera
woperekedwa ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Chipindulo chake nchiyani, abale anga,
munthu akanena, Ndili nacho
chikhulupiriro, koma alibe ntchito? Kodi
chikhulupirirocho chikhoza
kumpulumutsa?...chikhulupiriro,
chikapanda kukhala nacho ntchito,
chikhala chakufa m'kati mwakemo.
Yakobo 2:14-17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi