Ntchito Yachipulumutso Imene Atate Ahnsahnghong ndi Amai Akumwamba Amachita Ntchito yomaliza yachipulumutso yomwe idzakwaniritsidwa ndi Atate Ahnsahnghong amene anabwezeretsa choonadi cha pangano latsopano monga Adamu wauzimu, ndi Amai Akumwamba amene amatipatsa moyo wosatha monga Hava wauzimu.
Kodi Phwando la Ukwati wa Mwanawankhosa Limachitikira Kuti m'badwo wa Mzimu Woyera? Ndi Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse Mpingo wa Mulungu wokha umene umapereka uthenga wabwino wa chipulumutso cha Mulungu ku dziko lonse lapansi pouza anthu kuti achite nawo phwando la ukwati wa kumwamba lopangidwa ndi Mwanawankhosa ndi Mkazi Wake.
"Tiyeni tikondwere, tisekerere, ndipo tipereke ulemerero; pakuti ukwati wa Mwanawankhosa wafika, ndipo mkwatibwi wake wadzikonzekeretsa." Chivumbulutso 19:7
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi