Mulungu anapanga Baibulo ngati chikwangwani chosonyeza anthu kufika Kumwamba, komwe tikupita, ndipo anatiuza kuti timvere mawu a m’Baibulo.
Baibulo limatiphunzitsa kuti tsiku la Sabata ndi Paska ndi njira yopita Kumwamba.
Komabe, lero, mipingo yambiri amasunga kupembedza kwa lamlungu ndi Khrisimasi. Choncho, Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi anabwera kudzakonza chikwangwani.
. “Abale anga, phindu lake nʼchiyani ngati munthu anena kuti ali ndi chikhulupiriro koma chopanda ntchito? Kodi chikhulupiriro choterechi chingamupulumutse?... Chomwechonso, chikhulupiriro chokha chopanda ntchito ndi chakufa”
Yakobo 2:14–17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi