M’masiku amene mafumu ankalamulira, anthu amene ankaphwanya lamulo la mfumu ankaweruzidwa kuti aphedwe chifukwa choukira.
Momwemonso, n’kofunika kwambiri kutsatira zimene Baibulo limaphunzitsa—malamulo a Mulungu amene ndi Mfumu ya mafumu.
Choncho, Mpingo wa Mulungu umasunga pangano latsopano lolembedwa m’Baibulo monga tsiku la Sabata ndi Paskha.
Monga momwe aneneri ambiri monga Davide ndi Solomoni ankakonda Mulungu Yehova yekha m’nthawi ya Atate, komanso monga oyera mtima ndi Atumwi a Mpingo woyambirira amene ankakonda Yesu Khristu mu m’badwo wa Mwana, kukonda Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi mum’badwo wa Mzimu Woyera ndi chinsinsi cha chipulumutso.
[L]imene adzalionetsa m’nyengo za Iye yekha, amene ali Mwini Mphamvu wodala ndi wayekha, ndiye Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye; . . .
1 Timoteyo 6:15
Kufikira tsopano simunapemphe kanthu m’dzina langa; pemphani, ndipo mudzalandira, kuti chimwemwe chanu chikwaniridwe.
Yohane 16:24
Iye wakupambana, . . . ndipo ndidzalemba pa iye dzina la Mulungu wanga, ndi dzina la mzinda wa Mulungu wanga, la Yerusalemu watsopano, . . .ndi dzina langa latsopano.
Chivumbulutso 3:12
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi