Mpingo umene Mulungu mwini anaukhazikitsa ndi mwazi wake (mwazi wamtengo wapatali wa choonadi cha Paskha wa pangano la tsopano), mpingo umene umasunga tsiku lachisanu ndi chiwiri, tsiku la Sabata (Loweruka) kukhala lopatulika monga Yesu ndi ophunzira ake, ndi mpingo umene umabatiza anthu mdzina la Atate, la Mwana, ndi la Mzimu Woyera ku chikhululukiro cha machimo ndi Mpingo wa Mulungu kumene Mulungu ali nafe, ndipo amatipatsa chipulumutso monga Baibulo limafitokodzera umboni.
Anthu amene adzapulumutsidwe ali ndi pangano latsopano monga tsiku la Sabata la kwa Mulungu ndi Paskha m’mitima yawo. Adzazindikira ndi kulandira Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, omwe ali Mzimu ndi Mkwatibwi, ndikuchita ntchito yawo ngati ana akumwamba, ndiko kuphunzitsa dziko lapansi chomwe chili cholakwika ndi cholondola.
Paulo, woitanidwa akhale mtumwi wa Khristu Yesu mwa chifuniro cha Mulungu, ndi Sostene mbaleyo, kwa Mpingo wa Mulungu wakukhala mu Korinto, . . .
1 Akorinto 1:1–2
“Chifukwa chake anthu anga adzadziwa dzina langa; chifukwa chake tsiku limenelo iwo adzadziwa kuti Ine ndine amene ndinena; taonani, ndine pano.”
Yesaya 52:5–6
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi