Mpingo woyambirira, womwe unkakhulupirira Yesu ngati Mulungu ndipo unasunga ndi kulalikira pangano latsopano, unali wotsutsana ndi Ayuda, koma kuchokera ku maganizo a Mulungu, unali mpingo woona.
Baibulo lokha ndilo muyezo wodziwira mpatuko. Tchalitchi chilichonse chomwe chimatsatira ziphunzitso zopangidwa ndi anthu zomwe sizipezeka m'Baibulo ndi mpatuko wotheratu ndipo pamapeto pake chidzawonongedwa.
Masiku ano, mpingo wokhawo umene umatsatira choonadi cha pangano latsopano lomwe Yesu adakhazikitsa zaka 2,000 zapitazo, kuphatikizapo Sabata ndi Paskha, ndi Mpingo wa Mulungu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi