Baibulo limalosera kuti Mzimu ndi Mkwatibwi adzapereka madzi a moyo m ‘badwo uno (Chiv 22:17).
Mzimu ndi Mulungu Atate.
Ndiyeno, kodi Mkwatibwi amene akuonekera ndi Mzimu ndikutipatsa madzi a moyo ndani?
“Idza kuno, ndidzakuonetsa mkwatibwi, mkazi wa Mwanawankhosa.’’ . . .
nandionetsa mzinda wopatulikawo, Yerusalemu, wotsika mu Mwamba. . . (Chiv 21:9–10)
Koma Yerusalemu wa kumwamba uli waufulu, ndiwo amai wathu. (Agal 4:26)
Mwanjira ina, popeza Mkwatibwi wa Mzimu ndiye Mulungu Amayi, titha kulandira madalitso a madzi amoyo tikalandira Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi omwe ndi Mzimu ndi Mkwatibwi.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi