Mipingo yomwe idakhazikitsidwa imagwiritsa ntchito vesi lakuti “Nidzapenya Mwana wa Munthu alinkudza pa mitambo ya kumwamba, ndi mphamvu ndi ulemerero waukulu,” (Mat 24:30) kukakamira kuti Khristu amene adzabwerenso kachiwiri sadzabwera m'thupi chifukwa Baibulo limanena kuti Iye adzabwera ndi ulemerero waukulu. Komabe, Yesu anakwaniritsa ulosi wa m'buku la Yesaya wakuti “ulemerero wa Yehova udzavumbulutsidwa,” (Yes 40:5) pobwera m'thupi lomwe silinali laulemerero pamaso pa anthu. Choncho, tikhoza kumvetsetsa kuti kulimbikira kwawo n'konama.
Okhawo amene alandira Khristu ndipo apulumutsidwa ndi omwe angazindikire ulemerero wa Khristu Wobweranso Kachiwiri amene amabwera mofanana ndi ife.
Ndipo Mau anasandulika thupi, nakhazikika pakati pa ife, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wonga wa wobadwa yekha wa Atate, wodzala ndi chisomo ndi choonadi. Yohane 1:14
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi