Ngati pali Mulungu mmodzi yekha, ayenera kutchulidwa m'modzi nthawi zonse. Komabe, m’Baibulo, amatchulidwanso mochuluka kuti, “Ife.”
Ngakhale lero, mawu oti “Ife” akadali chinsinsi kwa akatswiri a Baibulo, koma Khristu Ahnsahnghong anavumbula tanthauzo lake lobisika.
Mulungu, wolenga mwamuna ndi mkazi m’chifaniziro chake, wopereka moyo wosatha m'badwo wa Mzimu Woyera, ndiye Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi