Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi, amene ali Mzimu ndi Mkwatibwi, anayamba kulenga zinthu pamodzi ndipo adzamaliza kulenga pamodzi.
Iwo amene samvetsa chisamaliro cha chipulumutso amanena kuti Mariya kapena oyera mtima ndi Mkwatibwi.
Komabe, Namwali Mariya kapena oyera sangakhale Mkwatibwi mu Chivumbulutso 22 chifukwa Iye ndi Mkazi wa Yesu ndi Iye amene amatipatsa madzi a moyo.
Mzimu ndi Mkwatibwi amene amatipatsa madzi a moyo mu m ‘bado wa Mzimu Woyera ndi Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi