Moyo wa thupi umathera mu imfa, ndipo pambuyo pake, kutengera zochita za munthu padziko lapansi lino, adzaweruzidwa molingana ndi Baibulo ndipo adzatumizidwa ku gehena.
Komabe, Baibulo limati iwo ochita nawo pa kuuka koyamba, posunga Paska wa pangano latsopano, mwambo wodya thupi ndi kumwa mwazi wa Yesu, ndi apadera ndipo sadzaweruzidwa.
Khristu Wobwera Kachiwiri Ahnsahnghong analonjeza kukhululukira machimo onse kudzera mu Paska, ndipo anatilola kutenga nawo mbali mu kuuka koyamba popanda kuweruzidwa, natipatsa dalitso la moyo wosatha ndi mwayi wolowa kumwamba.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi