Cholinga cha chikhulupiriro chathu ndi chipulumutso cha miyoyo yathu. kutanthauza kumasulidwa ku imfa yosatha ndi kuzunzika ku gehena, zomwe tinayenera kukumana nazo chifukwa cha machimo omwe tinachita kumwamba, ndi kulandira moyo wosatha.
Kudzera mu Paska, Mulungu anapatsa moyo wosatha kwaulere kwa anthu omvetsa chisoni omwe anayenera kufa.
Mpingo wa Mulungu uli ndi dalitso lolonjezedwa la moyo wosatha, kumene mamembala amadya mkate wa Paska ndi kumwa vinyo wa Paska, kuyimira thupi ndi mwazi wa Yesu, mogwirizana ndi ziphunzitso za m'Baibulo.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi