Pamene sayansi inakula, anthu anapeza mfundo za sayansi monga Dziko Lapansi lalenjekedwa pachabe, kuzungulira kwa Dzuwa, kapangidwe ka Dziko Lapansi, ndi kusithakwa madzi.
Komabe, Baibulo linalemba kale zinthu zimenezi zaka 3,500 zapitazo.
Ndi chifukwa Baibulo ndi mbiri ya Mulungu Mlengi amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo.
Ndiye n 'chifukwa chiyani Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi anapereka Baibulo kwa anthu?
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi