Mu nthawi ya Mpingo oyambirira, mtanda unali chida chophera anthu ndi fano loimira chikunja. Komabe, kuyambira nthawi ya Constantine, mtanda unkagwiritsidwa ntchito ndi Akhristu ngati chizindikiro.
Ngakhale masiku ano, anthu amene amapanga mtanda ndi kuulambira adzawonongedwa. Motero, tiyenera kukhulupirira pangano latsopano lomwe linakhazikitsidwa ndi Khristu, ndi kupulumutsidwa.
Mipingo yambiri padziko lonse lapansi ili ndi mtanda, koma Mpingo wa Mulungu wokha ndi umene umakana fanolo ndi kusunga pangano latsopano.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi