Akhristu ambiri masiku ano amakhulupirira kuti kuli Mulungu Atate
yekha, koma malemba oyambirira a m'Baibulo amanena kuti Mulungu ndi Elohim.
Zikutanthauza kuti sikuli Mulungu Atate okha.
Mpingo wa Mulungu umakhulupirira Mulungu Elohim,
Khristu Wobwera Kachiwiri Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Ndipo anati Mulungu, Tipange munthu m'chifanizo chathu, monga mwa chikhalidwe chathu: . . .
Mulungu ndipo adalenga munthu m'chifanizo chake, m'chifanizo cha Mulungu adamlenga iye;
adalenga iwo mwamuna ndi mkazi.
Genesis 1: 26-27
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi