Kuti tilandire madalitso a unsembe wachifumu Kumwamba monga momwe Mulungu adatilonjezera, tiyenera kupirira mpaka kumapeto ngakhale zitakhala bwanji, monganso tiyenera kuyembekezera kwa zaka zingapo kuti ubereke zipatso tikabzala mtengo.
Popeza Mulungu adatiphunzitsa kuphunzira pa zomwe zidachitikira Esau, Yobu, Mose, ndi Aaron, mamembala a Mpingo wa Mulungu amasunga chikhulupiriro chawo moyamikira komanso kuleza mtima pomvera mawu a Mulungu.
Inu mungogwiritsa zimene munaphunzira basi, mpaka Ine ndidzabwere. Amene adzapambana ndi kuchita chifuniro changa mpaka kumapeto, ndidzamupatsa ulamuliro pa mitundu yonse ya anthu. Civumbulutso 2:25–26
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi