Munthawi ya mafumu a Zhou, mkazi wa Jiang Taigong sakanakhoza kukhala mfumukazi chifukwa sanathe kupirira mavuto mpaka kumapeto koma adasiya mwamuna wake panjira.
Momwemonso, munjira yathu ya chikhulupiriro, okhawo omwe atsala ndi Mulungu mu Ziyoni mpaka kumapeto adzalandira madalitso a Kumwamba kwamuyaya kumene Mulungu adalonjeza.
Pofuna kugonjetsa mayesero a Satana amene amatitsogolera ku njira ya chiwonongeko ndi kukhala wopambana mu chikhulupiriro chathu, tiyenera nthawi zonse kukhala m'mawu a Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
“Potsiriza ndikuti, dzilimbitseni mwa Ambuye ndi mwa mphamvu zake zazikulu. Valani zida zonse za Mulungu kuti muthe kuyima ndi kukana machenjerero a Satana.” Aefeso 6:10–11
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi