Aliyense akabadwa, ayenera kukumana
ndi imfa kenako apatsidwe moyo
pambuyo pa tsiku limenelo.
Mulungu amaweruza amene adzazunzidwe ku
gehena ndi amene adzalandire ulemerero
kumwamba, malingana ndi ngati anakhala
mogwirizana ndi chifuniro cha
Mulungu padziko lapansi pano kapena ayi.
Baibulo, kuyambira Genesis mpaka
Chivumbulutso, limachitira umboni za
Mulungu Amayi, komanso m’Baibulo
loyambirira lachihebri,
linalembedwa kuti “Milungu [Elohim].”
Choncho, kutsatira ziphunzitso zones
za m ‘Baibulo ndi chifuniro cha
Mulungu, mamembala a Mpingo
wa Mulungu amakhulupirira Mulungu Elohim.
Ndipo popeza kwaikikatu kwa
anthu kufa kamodzi, ndipo atafa, chiweruziro; . . .
Ahebri 9:27
Si yense wakunena kwa Ine, Ambuye,
Ambuye, adzalowa mu Ufumu wa
Kumwamba; koma wakuchitayo
chifuniro cha Atate wanga wa Kumwamba.
Mateyu 7:21
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi