M’mbiri ya mikate isanu ndi nsomba
ziwiri, Mulungu ananena kuti mkate
wozizwitsa umene unadyetsa anthu
5,000 ndi chakudya chimene chimawonongeka.
Ndiponso, Iye anati mana ozizwitsa
amene anaperekedwa paulendo
wa zaka 40 m’chipululu ndi chakudya
chimene chimawasiyabe kufa
ngakhale kuti anachidya.
Komabe, popeza kuti mkate weniweni
wa Paska ndi Yesu, ananena
kuti ichi ndi chakudya
chopatsa moyo wosatha.
M’dziko la zozizwitsa, palibe chimene
chingachitike ndi luso la munthu.
Ali m’chipululu, azondi khumi aja
anazonda dziko la Kanani,
akumangoganizira zimene iwo akanachita.
Komabe, Yoswa ndi Kalebe anaganiza
zimene Mulungu akanatha kuchita.
Monga Yoswa ndi Kalebe, Mpingo wa
Mulungu umalalikira uthenga wabwino
wa pangano latsopano padziko lonse
lapansi, podalira mphamvu ya Khristu
Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Ine ndine mkate wamoyo.
Makolo anu adadya m'chipululu, ndipo adamwalira.
Mkate wotsika Kumwamba ndi uwu,
kuti munthu akadyeko ndi kusamwalira.
Mkate wamoyo wotsika Kumwamba Ndine
amene. Ngati munthu wina akadyako
mkate umene, adzakhala ndi moyo kosatha.
(Welengani Yohane 6:48-51.)
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi