Yesu adauza ophunzira Ake kuti aphunzire kuchokera kumtengo wamkuyu kuti atidziwitse za nthawi yomwe Iye adzabwere padziko lapansi kudzera m’chiwonongeko ndi kudziyimiranso pawokha kwa Israeli zomwe zikufanizidwa ndi mtengo wa mkuyu.
Khristu Ahnsahnghong anakwaniritsa ulosi wa mtengo wamkuyu komanso ulosi wa Mfumu Davide. Anatidziwitsanso za Mulungu Amayi ku Ziyoni, yomwe adakhazikitsa kudzera m’Paskha wa Chipangano Chatsopano mu M’badwo wa Mzimu Woyera. Iye ndiye Mulungu amene adzatipulumutse.
“Koma phunzirani ndi mkuyu fanizo lake; pamene tsopano nthambi yake ili yanthete, niphuka masamba ake, muzindikira kuti dzinja liyandikira; 33chomwechonso inu, pamene mudzaona zimenezo, zindikirani kuti Iye ali pafupi, inde pakhomo.”Mateyu 24:32–33
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi