Mpingo wa Mulungu, umene umatumikira Mulungu, uli
ndi malamulo otumikiranawo Mulungu.
Mulungu ananena kuti lamulo lililonse la pangano
latsopano, monga tsiku la Sabata ndi Paskha,
ndi chizindikiro chofunika kwambiri cha kulowa mu
ufumu wa Mulungu.
M’kachisi weniweni wa Mulungu, malamulo a Mulungu
ayenera kutsatiridwa.
Yesu ananena kuti Iye ndi oyera mtima
ali “kachisi wa Mulungu.”
Kupyolera mu izi, anationetsa kuti ife, kachisi wa
Mulungu, tiyenera kusunga malamulo a Mulungu.
Kodi simudziwa kuti muli Kachisi wa Mulungu,
ndi kuti Mzimu wa Mulungu agonera
mwa inu?
Ngati wina aononga Kachisi wa Mulungu, ameneyo Mulungu
adzamuononga; pakuti Kachisi wa Mulungu ali wopatulika,
ameneyo ndi inu.
1 Akorinto 3:16-17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi