Aneneri anachitira umboni kuti Mulungu adzakhazikitsa Pangano Latsopano.
Baibulo limachitiranso umboni kuti anthu sangathe kulandira chipulumutso mwa njira ina kuposa
Paskha Pangano Latsopano lokhazikitsidwa ndi thupi ndi mwazi wa Yesu.
Tsopano yekhayo amene anapereka madalitso a chikhululukiro cha machimo
ndipo moyo wosatha kwa anthu ndi Khristu Ahnsahnghong.
Chifukwa chake Mpingo wa Mulungu umakhulupirira
kuti Khristu Ahnsahnghong ndi Khristu amene anabwera kachiwiri.
“Iye wakudya thupi langa ndi kumwa mwazi wanga ali nao moyo wosatha; ndipo Ine ndidzamuukitsa iye tsiku lomaliza.” [Yohane 6:54]
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi